@UwemmieB77205 Profile picture

Uwemmie🎭

@UwemmieB77205

🤡 philophobia 🧸✨🤎

Uwemmie🎭 Reposted

Mchimwene kwa Mchimwene: Osakwera njinga ya moto yomwe ili pa rank…. Ziyenda ndipo ukwere yomwe ikulowera komwe ukupita.. ka mtengo pang’ono

Tweet Image 1

Uwemmie🎭 Reposted

Kuchipinda kwanu Nkhuku ikuyikila mazira koma busy kulemba zama Zodiac sign pa Twitter pano.


Uwemmie🎭 Reposted

Kapezedwe kanga sikakundilora kumadya nzimbe osameza.


Uwemmie🎭 Reposted

Enafe zokangana ndi anthu on social media sitingakwanitse.. zofooka zathu ndizambili atha kutimalizapo🙌🏾


Uwemmie🎭 Reposted

I’m currently living one of the most boring lifestyle any young person should be living 😅


Uwemmie🎭 Reposted

Tonse tili ku Malawi basi mudzindiimbila whatsapp call zoona? Mutu wanu umakoka?Mutakhala kuti muli kunja ndimvetsa even if it means a video call. Koma kunoko sitinafike pomayimbirana ma whatsapp call. Ngati ma units palibe, yesani *533# or *600#. That's the reason why you blush.


Uwemmie🎭 Reposted

Realized i have no one to talk to when im down even if its the closest person i let my problems eat me up i hope one day it doesn't get worse.


Uwemmie🎭 Reposted

Kubwera ku church, whole time muli pa phone, nde mmadzatani?


United States Trends
Loading...

Something went wrong.


Something went wrong.